Yehova ali wolungama; pakuti ndapikisana ndi m'kamwa mwace:Mudtvetu, mitundu ya anthu nonsenu, nimuone cisoni canga;Anamwali ndi anyamata anga atha kulowa m'ndende.