Yehova adzalikha munthu wakucita ici, wogalamutsa ndi wobvomereza m'tnahema a Yakobo, ndi iye wopereka copereka kwa Yehova wa makamu.