Yehova, ndinamva mbiri yanu ndi mantha;Yehova, tsitsimutsani nchito yanu pakati pa zaka,Pakati pa zaka mudziwitse;Pa mkwiyo mukumbukile cifundo.