Genesis 46:1-2 Buku Lopatulika 1992 (BL92) Ndipo Israyeli anamuka ulendo wace ndi zonse anali nazo, nafika ku Beereseba, napereka nsembe kwa Mulungu wa Isake