Ndipo anafunsa iwo za ubwino wao, nati, Kodi atate wanu ali ndi moyo? wokalamba uja amene nunanena uja: kodi alipo?