Ndipo Labani anati kwa Yakobo, Cifukwa iwe ndiwe mbale wanga, kodi udzanditumikira ine kwacabe? Undiuze ine, malipiro ako adzakhala otani?