Genesis 17:26-27 Buku Lopatulika 1992 (BL92) Tsiku lomwelo anadulidwa Abrahamu ndi Ismayeli mwana wace. Ndipo amuna onse a m'nyumba mwace obadwa m'nyumba, ndi