Ezekieli 31:1-2 Buku Lopatulika 1992 (BL92) Ndipo kunali caka cakhumi ndi cimodzi, mwezi wacitatu, tsiku loyamba la mwezi, anandidzera mau a Yehova, akuti,