32. Benjamini, Maluki, Semariya.
33. A ana a Hasumu: Matenai, Matata. Zabadi, Elifeleti, Yeremai, Manase, Simei.
34. A ana a Bani: Madai, Amiramu, ndi Ueli,
35. Benaya, Bedeya, Kelui,
36. Vaniya, Meremoti, Eliasibi,
37. Mataniya, Matenai, ndi Yasu,
38. ndi Bani, ndi Binui, Simei,
39. ndi Selemiya, ndi Natani, ndi Adaya,
40. Makinadebai, Sasai, Sarai,
41. Azareli, ndi Seleimiya, Semariya,
42. Salumu, Amariya, Yosefe.
43. A ana a Nebo: Yeieli, Matitiya, Zabadi, Zebina, Ido, ndi Yoeli, Banaya,
44. Awa onse adatenga akazi acilendo, ndi ena a iwowa anali ndi akazi amene adawabalira ana.