26. Ndi a ana a Elamu: Mataniya, Zekariya, ndi Yehieli, ndi Abidi, ndi Yeremoti, ndi Eliya.
27. Ndi a ana a Zatu: Elioenai, Eliasibi, Mataniya, ndi Yeremoti, ndi Zabadi, ndi Aziza.
28. Ndi a ana a Bebai: Yehohanana, Hananiya, Zabai, Atilai.
29. Ndi a ana a Bani: Mesulamu, Makuli, ndi Adaya, Yasubi, ndi Seali, Yeremoti.
30. Ndi a ana a Pahati: Moabu, Adina, ndi Kelali, Benaya, Maseya, Mataniya, Bezaleli, ndi Binui, ndi Manase.
31. Ndi a ana a Harimu: Eliezere, Isiya, Malikiya, Semaya, Simeoni,
32. Benjamini, Maluki, Semariya.
33. A ana a Hasumu: Matenai, Matata. Zabadi, Elifeleti, Yeremai, Manase, Simei.