Kuwerenga kwace ndiko: mbizi zagolidi makumi atatu, mbizi zasiliva cikwi cimodzi, mipeni makumi awiri mphambu isanu ndi inai;