Taona, mawa monga nthawi yino ndidzabvumbitsa mbvumbi wa matalala, sipadakhala unzace m'Aigupto kuyambira tsiku lija lidakhazikika kufikira lero lino.