Ndipo anapanga magango makumi asanu m'mphepete mwa nsaru imodzi, ya kuthungo, ya cilumikizano, naika magango makumi asanu m'mphepete mwa nsaru ya kuthungo, ya cilumikizano cina.