Eksodo 24:17-18 Buku Lopatulika 1992 (BL92) Ndipo maonekedwe a ulemerero wa Yehova anali ngati mota wonyeketsa pamwamba pa phiri, pamaso pa ana a Israyeli.