Mudzawafikitsa, ndi kuwaoka pa phiri la colowa canu,Pamalo pamene munadzipangira mukhalepo, Yehova,Malo oyera, amene manja anu, Ambuye, adakhazikika.