Mwa cifundo canu mwatsogolera anthu amene mudawaombola;Mwa mphamvu yanu mudawalondolera njira yakumka pokhala panu poyera.