Pakuti mpesa wao ndiwo wa ku Sodomu,Ndi wa m'minda ya ku Gomora;Mphesa zao ndizo mphesa zandulu,Matsangwi ao ngowawa.