Mmodzi akadapitikitsa zikwi,Awiri akadathawitsa zikwi khumi,Akadapanda kuwagulitsa Thanthwelao,Akadapanda kuwapereka Yehova.