Ndipo Elisa mneneriyo anaitana mmodzi wa ana a aneneri, nanena naye, Udzimangire m'cuuno, nutenge nsupa iyi ya mafuta m'dzanja mwako, numuke ku Ramoti Gileadi.