Nacita coipa pamaso pa Yehova, sanaleka zolakwa za Yerobiamu mwana wa Nebati, zimene analakwitsa nazo Israyeli.