Ndipo mkaziyo anali ndi mwana wa ng'ombe wonenepa m'nyumbamo; ndipo anafulumira, namupha, natenga ufa naukanyanga mkate wopanda cotupitsa;